Quran with Chichewa translation - Surah sad ayat 25 - صٓ - Page - Juz 23
﴿فَغَفَرۡنَا لَهُۥ ذَٰلِكَۖ وَإِنَّ لَهُۥ عِندَنَا لَزُلۡفَىٰ وَحُسۡنَ مَـَٔابٖ ﴾
[صٓ: 25]
﴿فغفرنا له ذلك وإن له عندنا لزلفى وحسن مآب﴾ [صٓ: 25]
Khaled Ibrahim Betala “Choncho tidamkhululukira iye zimenezo; ndithu iye ali nawo ulemelero kwa Ife ndi mabwelero abwino |