×

Iwe Davide! Ndithudi Ife takukhazika iwe kukhala Kazembe padziko lapansi motero weruza 38:26 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah sad ⮕ (38:26) ayat 26 in Chichewa

38:26 Surah sad ayat 26 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah sad ayat 26 - صٓ - Page - Juz 23

﴿يَٰدَاوُۥدُ إِنَّا جَعَلۡنَٰكَ خَلِيفَةٗ فِي ٱلۡأَرۡضِ فَٱحۡكُم بَيۡنَ ٱلنَّاسِ بِٱلۡحَقِّ وَلَا تَتَّبِعِ ٱلۡهَوَىٰ فَيُضِلَّكَ عَن سَبِيلِ ٱللَّهِۚ إِنَّ ٱلَّذِينَ يَضِلُّونَ عَن سَبِيلِ ٱللَّهِ لَهُمۡ عَذَابٞ شَدِيدُۢ بِمَا نَسُواْ يَوۡمَ ٱلۡحِسَابِ ﴾
[صٓ: 26]

Iwe Davide! Ndithudi Ife takukhazika iwe kukhala Kazembe padziko lapansi motero weruza pakati pa anthu mwachilungamo, ndipo usatsatire zilakolako za mtima wako chifukwa zidzakusocheretsa ku njira ya Mulungu. Ndithudi iwo amene asochera ku njira ya Mulungu adzalangidwa kwambiri chifukwa iwo amaiwala za tsiku lachiweruzo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ياداود إنا جعلناك خليفة في الأرض فاحكم بين الناس بالحق ولا تتبع, باللغة نيانجا

﴿ياداود إنا جعلناك خليفة في الأرض فاحكم بين الناس بالحق ولا تتبع﴾ [صٓ: 26]

Khaled Ibrahim Betala
““E iwe Daud! Ndithu ife takuchita iwe kukhala woyang’anira pa dziko; choncho weruza pakati pa anthuwa mwachilungamo; ndipo usatsatire zilakolako kuopa kuti zingakusokeretse ku njira ya Allah.” Ndithu amene akusokera ku njira ya Allah (potsatira zilakolako zawo), chilango chaukali chili pa iwo chifukwa cha kuiwala kwawo tsiku la chiwerengero
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek