Quran with Chichewa translation - Surah sad ayat 27 - صٓ - Page - Juz 23
﴿وَمَا خَلَقۡنَا ٱلسَّمَآءَ وَٱلۡأَرۡضَ وَمَا بَيۡنَهُمَا بَٰطِلٗاۚ ذَٰلِكَ ظَنُّ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْۚ فَوَيۡلٞ لِّلَّذِينَ كَفَرُواْ مِنَ ٱلنَّارِ ﴾
[صٓ: 27]
﴿وما خلقنا السماء والأرض وما بينهما باطلا ذلك ظن الذين كفروا فويل﴾ [صٓ: 27]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo sitidalenge thambo ndi nthaka ndi zapakati pake popanda cholinga. Zoterezo ndi maganizo a amene sadakhulupirire. Choncho kuonongeka kwakukulu ku Moto kuli kwa iwo amene sadakhulupirire |