Quran with Chichewa translation - Surah sad ayat 51 - صٓ - Page - Juz 23
﴿مُتَّكِـِٔينَ فِيهَا يَدۡعُونَ فِيهَا بِفَٰكِهَةٖ كَثِيرَةٖ وَشَرَابٖ ﴾
[صٓ: 51]
﴿متكئين فيها يدعون فيها بفاكهة كثيرة وشراب﴾ [صٓ: 51]
Khaled Ibrahim Betala “(Azidzakhala m’menemo) uku atatsamira (makama amtengo wapatali, ndipo adzakhala akusangalala) akuitanitsa mmenemo zipatso ndi zakumwa zambiri |