×

Ili ndi gulu la nkhondo limene lili kulowa ndi inu! Palibe kulandiridwa 38:59 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah sad ⮕ (38:59) ayat 59 in Chichewa

38:59 Surah sad ayat 59 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah sad ayat 59 - صٓ - Page - Juz 23

﴿هَٰذَا فَوۡجٞ مُّقۡتَحِمٞ مَّعَكُمۡ لَا مَرۡحَبَۢا بِهِمۡۚ إِنَّهُمۡ صَالُواْ ٱلنَّارِ ﴾
[صٓ: 59]

Ili ndi gulu la nkhondo limene lili kulowa ndi inu! Palibe kulandiridwa kwabwino kwa iwo! Ndithudi iwo adzalowa kumoto

❮ Previous Next ❯

ترجمة: هذا فوج مقتحم معكم لا مرحبا بهم إنهم صالو النار, باللغة نيانجا

﴿هذا فوج مقتحم معكم لا مرحبا بهم إنهم صالو النار﴾ [صٓ: 59]

Khaled Ibrahim Betala
“(Kudzanenedwa kwa opyola malire, omwe ndiatsogoleri a opembedza mafano): “Gulu ili lalikulu, lilowa nanu ku Moto; (omwe adali okutsatirani. Ndipo atsogoleri adzati): Siolandiridwa (mwamtendere). Ndithu iwo ngolowa ku Moto.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek