Quran with Chichewa translation - Surah sad ayat 62 - صٓ - Page - Juz 23
﴿وَقَالُواْ مَا لَنَا لَا نَرَىٰ رِجَالٗا كُنَّا نَعُدُّهُم مِّنَ ٱلۡأَشۡرَارِ ﴾
[صٓ: 62]
﴿وقالوا ما لنا لا نرى رجالا كنا نعدهم من الأشرار﴾ [صٓ: 62]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo (anthu a ku Moto) adzanena: “Kodi nchifukwa ninji sitikuwaona anthu aja omwe timawawerengera kuti ngoipa (pa dziko lapansi) |