×

Mulungu watumiza uthenga wabwino, Buku limene limabwerezabwereza chiphunzitso chake mosiyanasiyana. MatupiaiwoameneamaopaAmbuyewawo, amanjenjemera 39:23 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Az-Zumar ⮕ (39:23) ayat 23 in Chichewa

39:23 Surah Az-Zumar ayat 23 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zumar ayat 23 - الزُّمَر - Page - Juz 23

﴿ٱللَّهُ نَزَّلَ أَحۡسَنَ ٱلۡحَدِيثِ كِتَٰبٗا مُّتَشَٰبِهٗا مَّثَانِيَ تَقۡشَعِرُّ مِنۡهُ جُلُودُ ٱلَّذِينَ يَخۡشَوۡنَ رَبَّهُمۡ ثُمَّ تَلِينُ جُلُودُهُمۡ وَقُلُوبُهُمۡ إِلَىٰ ذِكۡرِ ٱللَّهِۚ ذَٰلِكَ هُدَى ٱللَّهِ يَهۡدِي بِهِۦ مَن يَشَآءُۚ وَمَن يُضۡلِلِ ٱللَّهُ فَمَا لَهُۥ مِنۡ هَادٍ ﴾
[الزُّمَر: 23]

Mulungu watumiza uthenga wabwino, Buku limene limabwerezabwereza chiphunzitso chake mosiyanasiyana. MatupiaiwoameneamaopaAmbuyewawo, amanjenjemera ndi Bukulo. Ndipo makungu ndi mitima yawo imafewa akamakumbukira Mulungu. Chimenechindichochilangizo cha Mulungu. Iye amatsogolera ndi icho aliyense amene Iye wamufuna. Koma iye amene Mulungu amamusiya kuti asochere, alibe wina woti angamutsogolere

❮ Previous Next ❯

ترجمة: الله نـزل أحسن الحديث كتابا متشابها مثاني تقشعر منه جلود الذين يخشون, باللغة نيانجا

﴿الله نـزل أحسن الحديث كتابا متشابها مثاني تقشعر منه جلود الذين يخشون﴾ [الزُّمَر: 23]

Khaled Ibrahim Betala
“Allah wavumbulutsa nkhani yabwino zedi yomwe ndi buku logwirizana nkhani zake; (losasemphana). Lobwerezabwereza (malamulo ake). Makungu a omwe amaopa Mbuye wawo amanjenjemera ndi ilo. Kenako makungu awo ndi mitima yawo zimakhazikika pokumbukira Allah. Buku limeneli ndi chiongoko cha Allah; ndi ilo, akumuongola amene wamfuna. Ndipo amene Allah wamulekelera kuti asokere (chifukwa chonyozera kwake choona), sangakhale ndi womuongola (ndi ompulumutsa ku chionongeko)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek