×

Kodi iye amene Mulungu watsekula mtima wake kuti alowe Chisilamu ndi kuona 39:22 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Az-Zumar ⮕ (39:22) ayat 22 in Chichewa

39:22 Surah Az-Zumar ayat 22 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zumar ayat 22 - الزُّمَر - Page - Juz 23

﴿أَفَمَن شَرَحَ ٱللَّهُ صَدۡرَهُۥ لِلۡإِسۡلَٰمِ فَهُوَ عَلَىٰ نُورٖ مِّن رَّبِّهِۦۚ فَوَيۡلٞ لِّلۡقَٰسِيَةِ قُلُوبُهُم مِّن ذِكۡرِ ٱللَّهِۚ أُوْلَٰٓئِكَ فِي ضَلَٰلٖ مُّبِينٍ ﴾
[الزُّمَر: 22]

Kodi iye amene Mulungu watsekula mtima wake kuti alowe Chisilamu ndi kuona kuwala kochokera kwa Ambuye wake ndi wofanana ndi munthu wouma mtima? Iyayi! Tsoka kwa iwo amene mitima yawo ndi yolimba pokumbukira Mulungu. Ndipo iwo ndi olakwa kwambiri

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أفمن شرح الله صدره للإسلام فهو على نور من ربه فويل للقاسية, باللغة نيانجا

﴿أفمن شرح الله صدره للإسلام فهو على نور من ربه فويل للقاسية﴾ [الزُّمَر: 22]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi amene Allah watsekula chifuwa chake povomereza Chisilamu, kotero kuti iye akuyenda mkuunika kwa Mbuye wake, (angafanane ndi yemwe akunyozera kupenyetsetsa zisonyezo za Allah?) Kuonongeka kwakukulu kuli pa ouma mitima yawo posakumbukira Allah (ndi kulabadira Qur’an). Iwo ali m’kusokera koonekera
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek