×

Mulungu ali kupereka fanizo la kapolo amene ali ndi mabwana ambiri ndi 39:29 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Az-Zumar ⮕ (39:29) ayat 29 in Chichewa

39:29 Surah Az-Zumar ayat 29 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zumar ayat 29 - الزُّمَر - Page - Juz 23

﴿ضَرَبَ ٱللَّهُ مَثَلٗا رَّجُلٗا فِيهِ شُرَكَآءُ مُتَشَٰكِسُونَ وَرَجُلٗا سَلَمٗا لِّرَجُلٍ هَلۡ يَسۡتَوِيَانِ مَثَلًاۚ ٱلۡحَمۡدُ لِلَّهِۚ بَلۡ أَكۡثَرُهُمۡ لَا يَعۡلَمُونَ ﴾
[الزُّمَر: 29]

Mulungu ali kupereka fanizo la kapolo amene ali ndi mabwana ambiri ndi kapolo amene ali ndi bwana mmodzi yekha. Kodi anthu awiriwa ndi ofanana m’machitidwe awo? Ulemerero ukhale kwa Mulungu! Koma anthu ambiri sadziwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ضرب الله مثلا رجلا فيه شركاء متشاكسون ورجلا سلما لرجل هل يستويان, باللغة نيانجا

﴿ضرب الله مثلا رجلا فيه شركاء متشاكسون ورجلا سلما لرجل هل يستويان﴾ [الزُّمَر: 29]

Khaled Ibrahim Betala
“Allah wapereka fanizo la munthu wotumikira mabwana awiri omwe ngokangana pa za iye, ndi munthu yemwe akutumikira bwana mmodzi. Kodi awiriwa ngofanana? Kuyamikidwa konse nkwa Allah! Koma ambiri a iwo sadziwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek