×

Inde! Ndithudi ulangizi wanga unadza kwa inu koma inu munaukana. Inu munali 39:59 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Az-Zumar ⮕ (39:59) ayat 59 in Chichewa

39:59 Surah Az-Zumar ayat 59 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zumar ayat 59 - الزُّمَر - Page - Juz 24

﴿بَلَىٰ قَدۡ جَآءَتۡكَ ءَايَٰتِي فَكَذَّبۡتَ بِهَا وَٱسۡتَكۡبَرۡتَ وَكُنتَ مِنَ ٱلۡكَٰفِرِينَ ﴾
[الزُّمَر: 59]

Inde! Ndithudi ulangizi wanga unadza kwa inu koma inu munaukana. Inu munali kunyada ndipo munali m’gulu la anthu osakhulupirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: بلى قد جاءتك آياتي فكذبت بها واستكبرت وكنت من الكافرين, باللغة نيانجا

﴿بلى قد جاءتك آياتي فكذبت بها واستكبرت وكنت من الكافرين﴾ [الزُّمَر: 59]

Khaled Ibrahim Betala
“(Adzauzidwa: “Nchiyani iwe?) Ndithu zidakufika zisonyezo Zanga, ndipo udazitsutsa ndi kudzitukumula; ndipo udali mmodzi wa okanira.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek