×

Iwo akhoza kudzibisa kwa anthu koma sangathe kudzibisa kwa Mulungu chifukwa Iye 4:108 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:108) ayat 108 in Chichewa

4:108 Surah An-Nisa’ ayat 108 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 108 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿يَسۡتَخۡفُونَ مِنَ ٱلنَّاسِ وَلَا يَسۡتَخۡفُونَ مِنَ ٱللَّهِ وَهُوَ مَعَهُمۡ إِذۡ يُبَيِّتُونَ مَا لَا يَرۡضَىٰ مِنَ ٱلۡقَوۡلِۚ وَكَانَ ٱللَّهُ بِمَا يَعۡمَلُونَ مُحِيطًا ﴾
[النِّسَاء: 108]

Iwo akhoza kudzibisa kwa anthu koma sangathe kudzibisa kwa Mulungu chifukwa Iye ali pamodzi ndi iwo pamene akonza chiwembu nthawi ya usiku ndi mawu amene samukondweretsa. Ndipo Mulungu amadziwa zimene iwo amachita

❮ Previous Next ❯

ترجمة: يستخفون من الناس ولا يستخفون من الله وهو معهم إذ يبيتون ما, باللغة نيانجا

﴿يستخفون من الناس ولا يستخفون من الله وهو معهم إذ يبيتون ما﴾ [النِّسَاء: 108]

Khaled Ibrahim Betala
“Akudzibisa kwa anthu (pochita za machimo) koma sakuzibisa kwa Allah pomwe Iye adali nawo pamodzi pamene adali kupangana usiku mawu osakondweretsa. Allah akudziwa bwinobwino zimene akuchita
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek