×

Koma iwo amene amakhulupirira ndipo amachita ntchito zabwino, tidzawalowetsa ku Minda yothiriridwa 4:122 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:122) ayat 122 in Chichewa

4:122 Surah An-Nisa’ ayat 122 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 122 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿وَٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ وَعَمِلُواْ ٱلصَّٰلِحَٰتِ سَنُدۡخِلُهُمۡ جَنَّٰتٖ تَجۡرِي مِن تَحۡتِهَا ٱلۡأَنۡهَٰرُ خَٰلِدِينَ فِيهَآ أَبَدٗاۖ وَعۡدَ ٱللَّهِ حَقّٗاۚ وَمَنۡ أَصۡدَقُ مِنَ ٱللَّهِ قِيلٗا ﴾
[النِّسَاء: 122]

Koma iwo amene amakhulupirira ndipo amachita ntchito zabwino, tidzawalowetsa ku Minda yothiriridwa ndi mitsinje ya madzi yoyenda pansi pake ndipo kumeneko adzakhalako mpaka kalekale. Lonjezo la Mulungu ndi loona. Kodi ndani amene anganene zoona kuposa Mulungu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: والذين آمنوا وعملوا الصالحات سندخلهم جنات تجري من تحتها الأنهار خالدين فيها, باللغة نيانجا

﴿والذين آمنوا وعملوا الصالحات سندخلهم جنات تجري من تحتها الأنهار خالدين فيها﴾ [النِّسَاء: 122]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo omwe akhulupirira ndi kumachita zabwino, tidzawalowetsa ku Minda yomwe pansi (ndi patsogolo) pake mitsinje ikuyenda. Adzakhala m’menemo muyaya. Ili ndilonjezo loona la Allah. Kodi ndani woona ponena kuposa Allah
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek