×

Ndipo mwini wake wa zonse za m’mlengalenga ndi za pa dziko lapansi 4:131 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:131) ayat 131 in Chichewa

4:131 Surah An-Nisa’ ayat 131 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 131 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿وَلِلَّهِ مَا فِي ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَمَا فِي ٱلۡأَرۡضِۗ وَلَقَدۡ وَصَّيۡنَا ٱلَّذِينَ أُوتُواْ ٱلۡكِتَٰبَ مِن قَبۡلِكُمۡ وَإِيَّاكُمۡ أَنِ ٱتَّقُواْ ٱللَّهَۚ وَإِن تَكۡفُرُواْ فَإِنَّ لِلَّهِ مَا فِي ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَمَا فِي ٱلۡأَرۡضِۚ وَكَانَ ٱللَّهُ غَنِيًّا حَمِيدٗا ﴾
[النِّسَاء: 131]

Ndipo mwini wake wa zonse za m’mlengalenga ndi za pa dziko lapansi ndi Mulungu. Ndipo, Ife tidawalangiza iwo amene analandira Buku inu musadadze ndiponso ndi inu nomwe kuti muziopa Mulungu. Koma ngati mukana, ndithudi, Mulungu ndiye mwini wa zonse zimene zili m’mlengalenga ndi padziko lapansi. Mulungu sasowa chilichonse ndipo ndi otamandidwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولله ما في السموات وما في الأرض ولقد وصينا الذين أوتوا الكتاب, باللغة نيانجا

﴿ولله ما في السموات وما في الأرض ولقد وصينا الذين أوتوا الكتاب﴾ [النِّسَاء: 131]

Khaled Ibrahim Betala
“Zonse za kumwamba ndi pansi nza Allah. Ndithudi, tidawalangiza omwe adapatsidwa buku patsogolo panu ndi inunso kuti muopeni Allah. Koma ngati mungakane, ndithudi, zonse za kumwamba ndi pansi nza Allah. Ndipo Allah Ngokhupuka kwabasi Wotamandidwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek