×

Koma ngati iwo asiyana, Mulungu adzapereka zochuluka kwa aliyense wa iwo kuchokera 4:130 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:130) ayat 130 in Chichewa

4:130 Surah An-Nisa’ ayat 130 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 130 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿وَإِن يَتَفَرَّقَا يُغۡنِ ٱللَّهُ كُلّٗا مِّن سَعَتِهِۦۚ وَكَانَ ٱللَّهُ وَٰسِعًا حَكِيمٗا ﴾
[النِّسَاء: 130]

Koma ngati iwo asiyana, Mulungu adzapereka zochuluka kwa aliyense wa iwo kuchokera ku zinthu zake zambiri. Ndipo Mulungu ndi wopereka mowolowa manja kwa zolengedwa zake ndipo ndi Wanzeru

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإن يتفرقا يغن الله كلا من سعته وكان الله واسعا حكيما, باللغة نيانجا

﴿وإن يتفرقا يغن الله كلا من سعته وكان الله واسعا حكيما﴾ [النِّسَاء: 130]

Khaled Ibrahim Betala
“Koma ngati atalekana, Allah angalemeretse aliyense wa iwo kuchokera m’zabwino zake zochuluka ndipo Allah ali nazo zambiri, Ngwanzeru zakuya
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek