×

oh inu anthu okhulupirira! Khulupirirani mwa Mulungundi Mtumwiwakendi Bukulimenewavumbulutsa kwa Mtumwi wake 4:136 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:136) ayat 136 in Chichewa

4:136 Surah An-Nisa’ ayat 136 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 136 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلَّذِينَ ءَامَنُوٓاْ ءَامِنُواْ بِٱللَّهِ وَرَسُولِهِۦ وَٱلۡكِتَٰبِ ٱلَّذِي نَزَّلَ عَلَىٰ رَسُولِهِۦ وَٱلۡكِتَٰبِ ٱلَّذِيٓ أَنزَلَ مِن قَبۡلُۚ وَمَن يَكۡفُرۡ بِٱللَّهِ وَمَلَٰٓئِكَتِهِۦ وَكُتُبِهِۦ وَرُسُلِهِۦ وَٱلۡيَوۡمِ ٱلۡأٓخِرِ فَقَدۡ ضَلَّ ضَلَٰلَۢا بَعِيدًا ﴾
[النِّسَاء: 136]

oh inu anthu okhulupirira! Khulupirirani mwa Mulungundi Mtumwiwakendi Bukulimenewavumbulutsa kwa Mtumwi wake ndi Buku limene Iye adavumbulutsa kale ndipo aliyense amene sakhulupirira Mulungu, Angelo ake, Mabuku ake, Atumwi ake ndi tsiku lomaliza ndithudi wasokera

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ياأيها الذين آمنوا آمنوا بالله ورسوله والكتاب الذي نـزل على رسوله والكتاب, باللغة نيانجا

﴿ياأيها الذين آمنوا آمنوا بالله ورسوله والكتاب الذي نـزل على رسوله والكتاب﴾ [النِّسَاء: 136]

Khaled Ibrahim Betala
“E inu amene mwakhulupirira! Khulupirirani Allah ndi Mtumiki Wake, ndi buku lomwe analivumbulutsa pa Mtumiki Wake, ndi mabuku omwe adawavumbulutsa kale. Ndipo amene akane Allah, angelo Ake, mabuku Ake, atumiki Ake ndi tsiku lachimaliziro, ndiye kuti wasokera; kusokera konkera nako kutali
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek