×

Ndithudi iwo amene akhulupirira ndipo kenaka akana ndipo akhulupirira ndipo akananso ndipo 4:137 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:137) ayat 137 in Chichewa

4:137 Surah An-Nisa’ ayat 137 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 137 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿إِنَّ ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ ثُمَّ كَفَرُواْ ثُمَّ ءَامَنُواْ ثُمَّ كَفَرُواْ ثُمَّ ٱزۡدَادُواْ كُفۡرٗا لَّمۡ يَكُنِ ٱللَّهُ لِيَغۡفِرَ لَهُمۡ وَلَا لِيَهۡدِيَهُمۡ سَبِيلَۢا ﴾
[النِّسَاء: 137]

Ndithudi iwo amene akhulupirira ndipo kenaka akana ndipo akhulupirira ndipo akananso ndipo aonjezera kusakhulupirira, Mulungu sadzawakhululukira kapena kuwatsogolera kunjira ya choonadi

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن الذين آمنوا ثم كفروا ثم آمنوا ثم كفروا ثم ازدادوا كفرا, باللغة نيانجا

﴿إن الذين آمنوا ثم كفروا ثم آمنوا ثم كفروا ثم ازدادوا كفرا﴾ [النِّسَاء: 137]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithudi, amene adakhulupirira, kenako nkusakhulupirira, nadzakhulupiriranso, kenako nkusakhulupiriranso, naonjezera kusakhulupirira, Allah sadzawakhululukira, ndipo sadzawawongolera m’njira (yabwino)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek