×

oh inu anthu okhulupirira! Musasankhe anthu osakhulupirira kuti akhale abwenzi anu mmalo 4:144 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:144) ayat 144 in Chichewa

4:144 Surah An-Nisa’ ayat 144 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 144 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ لَا تَتَّخِذُواْ ٱلۡكَٰفِرِينَ أَوۡلِيَآءَ مِن دُونِ ٱلۡمُؤۡمِنِينَۚ أَتُرِيدُونَ أَن تَجۡعَلُواْ لِلَّهِ عَلَيۡكُمۡ سُلۡطَٰنٗا مُّبِينًا ﴾
[النِّسَاء: 144]

oh inu anthu okhulupirira! Musasankhe anthu osakhulupirira kuti akhale abwenzi anu mmalo mwa anthu okhulupirira. Kodi mukufuna kuika umboni woonekera kwa Mulungu wokutsutsani inu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ياأيها الذين آمنوا لا تتخذوا الكافرين أولياء من دون المؤمنين أتريدون أن, باللغة نيانجا

﴿ياأيها الذين آمنوا لا تتخذوا الكافرين أولياء من دون المؤمنين أتريدون أن﴾ [النِّسَاء: 144]

Khaled Ibrahim Betala
“E inu amene mwakhulupirira! Musawachite osakhulupirira kukhala abwenzi anu kusiya okhulupirira (Asilamu), kodi mukufuna kuti Allah akhale ndi umboni woonekera pa inu (kuti ndinu oyipa)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek