×

Ndithudi iwo amene sakhulupirira Mulungu ndi Atumwi ake ndipo afuna kusiyanitsa pakati 4:150 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:150) ayat 150 in Chichewa

4:150 Surah An-Nisa’ ayat 150 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 150 - النِّسَاء - Page - Juz 6

﴿إِنَّ ٱلَّذِينَ يَكۡفُرُونَ بِٱللَّهِ وَرُسُلِهِۦ وَيُرِيدُونَ أَن يُفَرِّقُواْ بَيۡنَ ٱللَّهِ وَرُسُلِهِۦ وَيَقُولُونَ نُؤۡمِنُ بِبَعۡضٖ وَنَكۡفُرُ بِبَعۡضٖ وَيُرِيدُونَ أَن يَتَّخِذُواْ بَيۡنَ ذَٰلِكَ سَبِيلًا ﴾
[النِّسَاء: 150]

Ndithudi iwo amene sakhulupirira Mulungu ndi Atumwi ake ndipo afuna kusiyanitsa pakati pa Mulungu ndi Atumwi ake ponena kuti: “Ife timakhulupirira mwa ena ndipo sitikhulupirira ena.” Ndipo amafuna kusankha njira yapakati ndi pakati

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن الذين يكفرون بالله ورسله ويريدون أن يفرقوا بين الله ورسله ويقولون, باللغة نيانجا

﴿إن الذين يكفرون بالله ورسله ويريدون أن يفرقوا بين الله ورسله ويقولون﴾ [النِّسَاء: 150]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithudi amene sakhulupirira Allah ndi atumiki Ake, ndikumafuna kulekanitsa pakati pa Allah ndi atumiki Ake, ndikumanena kuti: “Ena tikuwakhulupirira, koma ena tikuwakana,” ndikumafunanso kukhonza njira yapakati pa zimenezo
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek