×

Kaya inu muonetsera pochita zabwino kapena mubisa, kapena mukhululukira zoipa, ndithudi, Mulungu 4:149 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:149) ayat 149 in Chichewa

4:149 Surah An-Nisa’ ayat 149 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 149 - النِّسَاء - Page - Juz 6

﴿إِن تُبۡدُواْ خَيۡرًا أَوۡ تُخۡفُوهُ أَوۡ تَعۡفُواْ عَن سُوٓءٖ فَإِنَّ ٱللَّهَ كَانَ عَفُوّٗا قَدِيرًا ﴾
[النِّسَاء: 149]

Kaya inu muonetsera pochita zabwino kapena mubisa, kapena mukhululukira zoipa, ndithudi, Mulungu ndi wokhululukira ndi wamphamvu zonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن تبدوا خيرا أو تخفوه أو تعفوا عن سوء فإن الله كان, باللغة نيانجا

﴿إن تبدوا خيرا أو تخفوه أو تعفوا عن سوء فإن الله كان﴾ [النِّسَاء: 149]

Khaled Ibrahim Betala
“Ngati mungaonetse chabwino, kapena kuchibisa, kapena kukhululukira zoipa, (zoterozo ndizo zofunika), ndithu Allah Ngokhululuka ndiponso Ngokhoza
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek