×

Motero iwo amene ali ndi chikhulupiriro ndipo amachita ntchito zabwino, Iye adzawapatsa 4:173 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:173) ayat 173 in Chichewa

4:173 Surah An-Nisa’ ayat 173 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 173 - النِّسَاء - Page - Juz 6

﴿فَأَمَّا ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ وَعَمِلُواْ ٱلصَّٰلِحَٰتِ فَيُوَفِّيهِمۡ أُجُورَهُمۡ وَيَزِيدُهُم مِّن فَضۡلِهِۦۖ وَأَمَّا ٱلَّذِينَ ٱسۡتَنكَفُواْ وَٱسۡتَكۡبَرُواْ فَيُعَذِّبُهُمۡ عَذَابًا أَلِيمٗا وَلَا يَجِدُونَ لَهُم مِّن دُونِ ٱللَّهِ وَلِيّٗا وَلَا نَصِيرٗا ﴾
[النِّسَاء: 173]

Motero iwo amene ali ndi chikhulupiriro ndipo amachita ntchito zabwino, Iye adzawapatsa mphotho zawo mokwanira ndipo adzawalemeretsa iwo mwachisomo chake chochuluka. Koma iwo amene akana kupembedza kapena oyerekedwa, Iye adzawalanga ndi chilango chowawa. Ndipo iwo sadzapeza wina woposa Mulungu kuti awateteze kapena kuwathandiza

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فأما الذين آمنوا وعملوا الصالحات فيوفيهم أجورهم ويزيدهم من فضله وأما الذين, باللغة نيانجا

﴿فأما الذين آمنوا وعملوا الصالحات فيوفيهم أجورهم ويزيدهم من فضله وأما الذين﴾ [النِّسَاء: 173]

Khaled Ibrahim Betala
“Koma amene adamkhulupirira (Yesuyo) ndi kuchita zabwino adzawapatsa malipiro ao mokwanira ndi kuwaonjezera mu zabwino Zake. Koma amene adaona kunyozeka (pokhala kapolo wa Allah) nadzitukumula, adzawalanga chilango chowawa; ndipo sadzapeza bwenzi ngakhale mtetezi kupatula Allah
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek