×

Kulibe phindu kulapa kwa iwo amene amachita zinthu zoipa mpaka pamene imfa 4:18 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:18) ayat 18 in Chichewa

4:18 Surah An-Nisa’ ayat 18 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 18 - النِّسَاء - Page - Juz 4

﴿وَلَيۡسَتِ ٱلتَّوۡبَةُ لِلَّذِينَ يَعۡمَلُونَ ٱلسَّيِّـَٔاتِ حَتَّىٰٓ إِذَا حَضَرَ أَحَدَهُمُ ٱلۡمَوۡتُ قَالَ إِنِّي تُبۡتُ ٱلۡـَٰٔنَ وَلَا ٱلَّذِينَ يَمُوتُونَ وَهُمۡ كُفَّارٌۚ أُوْلَٰٓئِكَ أَعۡتَدۡنَا لَهُمۡ عَذَابًا أَلِيمٗا ﴾
[النِّسَاء: 18]

Kulibe phindu kulapa kwa iwo amene amachita zinthu zoipa mpaka pamene imfa imupeza wina wa iwo ndipo ati: “Tsopano ndalapa,” kapena kwa iwo amene amafa ali osakhulupirira. Kwa iwo Ife tawakonzera chilango chowawa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وليست التوبة للذين يعملون السيئات حتى إذا حضر أحدهم الموت قال إني, باللغة نيانجا

﴿وليست التوبة للذين يعملون السيئات حتى إذا حضر أحدهم الموت قال إني﴾ [النِّسَاء: 18]

Khaled Ibrahim Betala
“Kulapa sikungalandiridwe pa omwe akuchita zoipa mpaka imfa kumfikira m’modzi wa iwo (pamenepo) nkunena: “Ndithudi ine ndikulapa tsopano.” Ngakhalenso pa omwe akufa ali osakhulupirira. Iwo tawakonzera chilango chopweteka
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek