×

oh inu anthu okhulupirira! Inu simuloledwa kulowa chokolo chokakamiza ndipo musawazunze ndi 4:19 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:19) ayat 19 in Chichewa

4:19 Surah An-Nisa’ ayat 19 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 19 - النِّسَاء - Page - Juz 4

﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ لَا يَحِلُّ لَكُمۡ أَن تَرِثُواْ ٱلنِّسَآءَ كَرۡهٗاۖ وَلَا تَعۡضُلُوهُنَّ لِتَذۡهَبُواْ بِبَعۡضِ مَآ ءَاتَيۡتُمُوهُنَّ إِلَّآ أَن يَأۡتِينَ بِفَٰحِشَةٖ مُّبَيِّنَةٖۚ وَعَاشِرُوهُنَّ بِٱلۡمَعۡرُوفِۚ فَإِن كَرِهۡتُمُوهُنَّ فَعَسَىٰٓ أَن تَكۡرَهُواْ شَيۡـٔٗا وَيَجۡعَلَ ٱللَّهُ فِيهِ خَيۡرٗا كَثِيرٗا ﴾
[النِّسَاء: 19]

oh inu anthu okhulupirira! Inu simuloledwa kulowa chokolo chokakamiza ndipo musawazunze ndi cholinga choti muwalande zina zimene mudawapatsa pokhapokha ngati achita chigololo. Ndipo khalani nawo mwa mtendere. Ngati simukuwafuna, mwina mungachide chinthu chimene Mulungu waikamo zabwino zambiri

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ياأيها الذين آمنوا لا يحل لكم أن ترثوا النساء كرها ولا تعضلوهن, باللغة نيانجا

﴿ياأيها الذين آمنوا لا يحل لكم أن ترثوا النساء كرها ولا تعضلوهن﴾ [النِّسَاء: 19]

Khaled Ibrahim Betala
“E inu amene mwakhulupirira! Sikovomerezedwa kwa inu kuwalowa chokolo akazi mowakakamiza. Ndipo musawaletse (kukwatiwa ndi amuna ena) ndi cholinga choti muwalande zina mwa zomwe mudawapatsa, (nkosaloledwa kutero) kupatula ngati atachita choipa choonekera. Ndipo khalani nawo mwa ubwino. Ngati mutawada (musalekane nawo), mwina mungade chinthu chomwe Allah waika zabwino zambiri mkati mwake
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek