×

Mulungu amavomera kulapa kwa amene achita zoipa mosazindikira ngati alapa mwamsanga. Ndi 4:17 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:17) ayat 17 in Chichewa

4:17 Surah An-Nisa’ ayat 17 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 17 - النِّسَاء - Page - Juz 4

﴿إِنَّمَا ٱلتَّوۡبَةُ عَلَى ٱللَّهِ لِلَّذِينَ يَعۡمَلُونَ ٱلسُّوٓءَ بِجَهَٰلَةٖ ثُمَّ يَتُوبُونَ مِن قَرِيبٖ فَأُوْلَٰٓئِكَ يَتُوبُ ٱللَّهُ عَلَيۡهِمۡۗ وَكَانَ ٱللَّهُ عَلِيمًا حَكِيمٗا ﴾
[النِّسَاء: 17]

Mulungu amavomera kulapa kwa amene achita zoipa mosazindikira ngati alapa mwamsanga. Ndi iwo amene Mulungu adzawakhululukira ndipo Mulungu ndi wodziwa ndiponso wanzeru

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إنما التوبة على الله للذين يعملون السوء بجهالة ثم يتوبون من قريب, باللغة نيانجا

﴿إنما التوبة على الله للذين يعملون السوء بجهالة ثم يتوبون من قريب﴾ [النِّسَاء: 17]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithudi kulapa kovomerezeka ndi Allah nkwa omwe amachita zoipa mwa umbuli kenako nkulapa mwachangu. Amenewo ndiomwe Allah amawalandira kulapa kwawo. Ndipo Allah Ngodziwa kwambiri Ngwanzeru zakuya
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek