×

Inu mwaletsedwa kukwatira awa: Amayi anu, ana anu a akazi, alongo anu, 4:23 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:23) ayat 23 in Chichewa

4:23 Surah An-Nisa’ ayat 23 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 23 - النِّسَاء - Page - Juz 4

﴿حُرِّمَتۡ عَلَيۡكُمۡ أُمَّهَٰتُكُمۡ وَبَنَاتُكُمۡ وَأَخَوَٰتُكُمۡ وَعَمَّٰتُكُمۡ وَخَٰلَٰتُكُمۡ وَبَنَاتُ ٱلۡأَخِ وَبَنَاتُ ٱلۡأُخۡتِ وَأُمَّهَٰتُكُمُ ٱلَّٰتِيٓ أَرۡضَعۡنَكُمۡ وَأَخَوَٰتُكُم مِّنَ ٱلرَّضَٰعَةِ وَأُمَّهَٰتُ نِسَآئِكُمۡ وَرَبَٰٓئِبُكُمُ ٱلَّٰتِي فِي حُجُورِكُم مِّن نِّسَآئِكُمُ ٱلَّٰتِي دَخَلۡتُم بِهِنَّ فَإِن لَّمۡ تَكُونُواْ دَخَلۡتُم بِهِنَّ فَلَا جُنَاحَ عَلَيۡكُمۡ وَحَلَٰٓئِلُ أَبۡنَآئِكُمُ ٱلَّذِينَ مِنۡ أَصۡلَٰبِكُمۡ وَأَن تَجۡمَعُواْ بَيۡنَ ٱلۡأُخۡتَيۡنِ إِلَّا مَا قَدۡ سَلَفَۗ إِنَّ ٱللَّهَ كَانَ غَفُورٗا رَّحِيمٗا ﴾
[النِّسَاء: 23]

Inu mwaletsedwa kukwatira awa: Amayi anu, ana anu a akazi, alongo anu, azakhali anu, achemwali amayi anu, ana akazi achimwene anu, ana akazi a alongo anu, amayi amene adakuyamwitsani, akazi amene mudayamwitsidwa nawo bere limodzi, apongozi anu, ndi ana a akazi owapeza amene muli kuwasunga amene anabereka akazi amene mwawakwatira. Koma ngati simunagonepo ndi amai awo palibe choletsa kwa inu kuwakwatira atsikanawo. Kukwatiraakaziaanaanuamunaamenemudaberekainundi akazi awiri amimba imodzi nthawi imodzi ndi koletsedwa kupatula zimene zinachitika kale. Ndithudi Mulungu ndi okhululukira ndi wa chisoni chosatha

❮ Previous Next ❯

ترجمة: حرمت عليكم أمهاتكم وبناتكم وأخواتكم وعماتكم وخالاتكم وبنات الأخ وبنات الأخت وأمهاتكم, باللغة نيانجا

﴿حرمت عليكم أمهاتكم وبناتكم وأخواتكم وعماتكم وخالاتكم وبنات الأخ وبنات الأخت وأمهاتكم﴾ [النِّسَاء: 23]

Khaled Ibrahim Betala
“Kwaletsedwa kwa inu kukwatira amayi anu, ana anu, alongo anu, azakhali anu, amayi anu aang’ono kapena aakulu, ana achikazi am’bale wanu, ana achikazi a mlongo wanu, amayi anu amene adakuyamwitsani, alongo anu oberekedwa ndi amene adakuyamwitsanipo. Mayi a akazi anu, ana achikazi owapeza amene mukuwasunga woberekedwa ndi akazi anu omwe mwalowana nawo. Koma ngati simudalowane nawo, nkosaletsedwa kwa inu kukwatira ana awowo; ndi akazi a ana amuna omwe ngochokera kumisana yanu. Ndiponso nkoletsedwa kwa inu kukwatira mophatikiza mkazi ndi mchemwali wake obadwa naye, kupatula zomwe zidapita. Ndithudi Allah Ngokhululuka kwambiri Ngwachisoni zedi
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek