Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 22 - النِّسَاء - Page - Juz 4
﴿وَلَا تَنكِحُواْ مَا نَكَحَ ءَابَآؤُكُم مِّنَ ٱلنِّسَآءِ إِلَّا مَا قَدۡ سَلَفَۚ إِنَّهُۥ كَانَ فَٰحِشَةٗ وَمَقۡتٗا وَسَآءَ سَبِيلًا ﴾
[النِّسَاء: 22]
﴿ولا تنكحوا ما نكح آباؤكم من النساء إلا ما قد سلف إنه﴾ [النِّسَاء: 22]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo musakwatire akazi amene adakwatiwapo ndi atate anu, kupatula zomwe zidapita, (musabwerezenso kuzichita). Ndithudi, chinthu ichi nchauve ndipo nchodedwa ndiponso ndinjira yoipa |