×

Mulungu afuna kuti akufotokozereni inu ndi kukutsogolerani ku njira za iwo amene 4:26 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:26) ayat 26 in Chichewa

4:26 Surah An-Nisa’ ayat 26 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 26 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿يُرِيدُ ٱللَّهُ لِيُبَيِّنَ لَكُمۡ وَيَهۡدِيَكُمۡ سُنَنَ ٱلَّذِينَ مِن قَبۡلِكُمۡ وَيَتُوبَ عَلَيۡكُمۡۗ وَٱللَّهُ عَلِيمٌ حَكِيمٞ ﴾
[النِّسَاء: 26]

Mulungu afuna kuti akufotokozereni inu ndi kukutsogolerani ku njira za iwo amene adalipo inu musanadze ndi kukukhululukirani inu. Ndipo Mulungu ndi wodziwa ndi wanzeru

❮ Previous Next ❯

ترجمة: يريد الله ليبين لكم ويهديكم سنن الذين من قبلكم ويتوب عليكم والله, باللغة نيانجا

﴿يريد الله ليبين لكم ويهديكم سنن الذين من قبلكم ويتوب عليكم والله﴾ [النِّسَاء: 26]

Khaled Ibrahim Betala
“Allah akufuna kukufotokozerani ndi kukutsogolerani kunjira za omwe adalipo patsogolo panu; ndiponso akufuna kulandira kulapa kwanu. Ndipo Allah Ngodziwa kwambiri, Ngwanzeru zakuya
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek