×

Ndipo kwa aliyense tamuikira abale olandira chuma chimene chasiyidwa ndi makolo ndi 4:33 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:33) ayat 33 in Chichewa

4:33 Surah An-Nisa’ ayat 33 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 33 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿وَلِكُلّٖ جَعَلۡنَا مَوَٰلِيَ مِمَّا تَرَكَ ٱلۡوَٰلِدَانِ وَٱلۡأَقۡرَبُونَۚ وَٱلَّذِينَ عَقَدَتۡ أَيۡمَٰنُكُمۡ فَـَٔاتُوهُمۡ نَصِيبَهُمۡۚ إِنَّ ٱللَّهَ كَانَ عَلَىٰ كُلِّ شَيۡءٖ شَهِيدًا ﴾
[النِّسَاء: 33]

Ndipo kwa aliyense tamuikira abale olandira chuma chimene chasiyidwa ndi makolo ndi abale. Ndipo iwo amene mwachita nawo chipangano, apatseni gawo lawo nawonso kuti alandire. Ndithudi Mulungu ndi mboni pa zinthu zonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولكل جعلنا موالي مما ترك الوالدان والأقربون والذين عقدت أيمانكم فآتوهم نصيبهم, باللغة نيانجا

﴿ولكل جعلنا موالي مما ترك الوالدان والأقربون والذين عقدت أيمانكم فآتوهم نصيبهم﴾ [النِّسَاء: 33]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo anthu tawaikira alowa mmalo pa zomwe asiya makolo awiri ndi achibale. Ndipo amene mudagwirizana nawo chipangano, apatseni gawo lawo. Ndithudi, Allah Ndimboni pa chilichonse
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek