×

Ndipo musasirire zokoma zimene Mulungu wawapatsa ena a inu kuposa anzawo. Kwa 4:32 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:32) ayat 32 in Chichewa

4:32 Surah An-Nisa’ ayat 32 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 32 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿وَلَا تَتَمَنَّوۡاْ مَا فَضَّلَ ٱللَّهُ بِهِۦ بَعۡضَكُمۡ عَلَىٰ بَعۡضٖۚ لِّلرِّجَالِ نَصِيبٞ مِّمَّا ٱكۡتَسَبُواْۖ وَلِلنِّسَآءِ نَصِيبٞ مِّمَّا ٱكۡتَسَبۡنَۚ وَسۡـَٔلُواْ ٱللَّهَ مِن فَضۡلِهِۦٓۚ إِنَّ ٱللَّهَ كَانَ بِكُلِّ شَيۡءٍ عَلِيمٗا ﴾
[النِّسَاء: 32]

Ndipo musasirire zokoma zimene Mulungu wawapatsa ena a inu kuposa anzawo. Kwa amuna kuli gawo kuzimene amachita, nawonso akazi ali ndi gawo muzimene amachita ndipo mupempheni Mulungu kuti akupatseni zabwino zake. Ndithudi Mulungu amadziwa chinthu chilichonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولا تتمنوا ما فضل الله به بعضكم على بعض للرجال نصيب مما, باللغة نيانجا

﴿ولا تتمنوا ما فضل الله به بعضكم على بعض للرجال نصيب مما﴾ [النِّسَاء: 32]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo musazilakelake (mwadumbo) zomwe Allah wawadalitsa nazo ena mwa inu. Amuna ali ndi gawo (lokwanira) la zomwe apeza. Nawonso akazi ali ndi gawo (lokwanira) la zomwe apeza. Ndipo mpempheni Allah zabwino zake. Ndithudi, Allah Ngodziwa chilichonse
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek