×

Ndipo pamene auzidwa “Bwerani ku zimene Mulungu wavumbulutsa ndiponso kwa Mtumwi,” iwe 4:61 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:61) ayat 61 in Chichewa

4:61 Surah An-Nisa’ ayat 61 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 61 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿وَإِذَا قِيلَ لَهُمۡ تَعَالَوۡاْ إِلَىٰ مَآ أَنزَلَ ٱللَّهُ وَإِلَى ٱلرَّسُولِ رَأَيۡتَ ٱلۡمُنَٰفِقِينَ يَصُدُّونَ عَنكَ صُدُودٗا ﴾
[النِّسَاء: 61]

Ndipo pamene auzidwa “Bwerani ku zimene Mulungu wavumbulutsa ndiponso kwa Mtumwi,” iwe umaona anthu a chinyengo ali kukukana iwe mwamwano

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذا قيل لهم تعالوا إلى ما أنـزل الله وإلى الرسول رأيت المنافقين, باللغة نيانجا

﴿وإذا قيل لهم تعالوا إلى ما أنـزل الله وإلى الرسول رأيت المنافقين﴾ [النِّسَاء: 61]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo akauzidwa: “Idzani ku zomwe Allah wavumbulutsa, ndiponso (idzani) kwa Mtumiki.” Uwaona achinyengo akudziika kutali kwabasi ndi iwe
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek