×

Mulungu! Kulibe mulungu wina koma Iye yekha. Ndithudi Iye adzakusonkhanitsani nonse pamodzi 4:87 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:87) ayat 87 in Chichewa

4:87 Surah An-Nisa’ ayat 87 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 87 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿ٱللَّهُ لَآ إِلَٰهَ إِلَّا هُوَۚ لَيَجۡمَعَنَّكُمۡ إِلَىٰ يَوۡمِ ٱلۡقِيَٰمَةِ لَا رَيۡبَ فِيهِۗ وَمَنۡ أَصۡدَقُ مِنَ ٱللَّهِ حَدِيثٗا ﴾
[النِّسَاء: 87]

Mulungu! Kulibe mulungu wina koma Iye yekha. Ndithudi Iye adzakusonkhanitsani nonse pamodzi patsiku louka kwa akufa, tsiku lopanda chikaiko. Kodi ndani amalankhula zoona kuposa Mulungu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: الله لا إله إلا هو ليجمعنكم إلى يوم القيامة لا ريب فيه, باللغة نيانجا

﴿الله لا إله إلا هو ليجمعنكم إلى يوم القيامة لا ريب فيه﴾ [النِّسَاء: 87]

Khaled Ibrahim Betala
“Allah! Palibe wopembedzedwa mwa choonadi koma Iye basi. Ndithudi, adzakusonkhanitsani tsiku la chiweruziro lopanda chikaiko mwa ilo. Kodi ndani ali onena zoona kuposa Allah
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek