×

Ngati munthu akulonjerani onetsetsani kuti malonje anu ndi abwino kuposa malonje ake 4:86 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:86) ayat 86 in Chichewa

4:86 Surah An-Nisa’ ayat 86 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 86 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿وَإِذَا حُيِّيتُم بِتَحِيَّةٖ فَحَيُّواْ بِأَحۡسَنَ مِنۡهَآ أَوۡ رُدُّوهَآۗ إِنَّ ٱللَّهَ كَانَ عَلَىٰ كُلِّ شَيۡءٍ حَسِيبًا ﴾
[النِّسَاء: 86]

Ngati munthu akulonjerani onetsetsani kuti malonje anu ndi abwino kuposa malonje ake kapena mumubwezere monga momwe wakulonjererani. Ndithudi Mulungu amasunga chiwerengero cha zinthu zonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذا حييتم بتحية فحيوا بأحسن منها أو ردوها إن الله كان على, باللغة نيانجا

﴿وإذا حييتم بتحية فحيوا بأحسن منها أو ردوها إن الله كان على﴾ [النِّسَاء: 86]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo pamene mwalonjeredwa; kulonjeredwa kwamtundu uliwonse (Salam) vomerani ndi malonje abwino oposa amenewo, kapena bwezani ofanana nawo. Ndithudi, Allah Ngowerengera chinthu chilichonse
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek