×

NdipoIfetikadatumizaBukulaKoranimuchiyankhulo china osati Chiarabu, iwo akadanena kuti, “Kodi bwanji mawu ake sali 41:44 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Fussilat ⮕ (41:44) ayat 44 in Chichewa

41:44 Surah Fussilat ayat 44 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 44 - فُصِّلَت - Page - Juz 24

﴿وَلَوۡ جَعَلۡنَٰهُ قُرۡءَانًا أَعۡجَمِيّٗا لَّقَالُواْ لَوۡلَا فُصِّلَتۡ ءَايَٰتُهُۥٓۖ ءَا۬عۡجَمِيّٞ وَعَرَبِيّٞۗ قُلۡ هُوَ لِلَّذِينَ ءَامَنُواْ هُدٗى وَشِفَآءٞۚ وَٱلَّذِينَ لَا يُؤۡمِنُونَ فِيٓ ءَاذَانِهِمۡ وَقۡرٞ وَهُوَ عَلَيۡهِمۡ عَمًىۚ أُوْلَٰٓئِكَ يُنَادَوۡنَ مِن مَّكَانِۭ بَعِيدٖ ﴾
[فُصِّلَت: 44]

NdipoIfetikadatumizaBukulaKoranimuchiyankhulo china osati Chiarabu, iwo akadanena kuti, “Kodi bwanji mawu ake sali kufotokozeredwa bwinobwino? Chiyani! Chiyankhulo cha chilendo osati Chiarabu!” Nena, “Ilo ndi la iwo amene amakhulupirira, ndi chilangizo ndiponso mankhwala ochiritsa. Ndipo iwo amene sakhulupirira, makutu awo ndi ogontha ndipo ilo ndi khungu kwa iwo. Iwo ndiwo amene amaitanidwa kuchokera kutali.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولو جعلناه قرآنا أعجميا لقالوا لولا فصلت آياته أأعجمي وعربي قل هو, باللغة نيانجا

﴿ولو جعلناه قرآنا أعجميا لقالوا لولا فصلت آياته أأعجمي وعربي قل هو﴾ [فُصِّلَت: 44]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo tikadaichita Qur’an iyi kukhala mchiyankhulo chachilendo osati Chiarabu, akadanena: “Nchifukwa ninji ma Ayah ake sadafotokozedwe bwino; buku la chilankhulo chachilendo olalikidwa nkukhala mwarabu?” Nena (iwe Mtumiki): “Limeneli ndi chiongoko ndi chochiritsa kwa okhulupirira. Koma kwa amene salikhulupirira, (zili ngati kuti) mmakutu mwawo muli ugonthi (chifukwa cholinyoza) umene ukuwachititsa khungu (chifukwa choti saona chilichonse mmenemo chowapindulira), iwo (okanirawo ali ngati) akuitanidwa (ndi woitana) kuchokera pamtunda wapatali (kuti amkhulupirire).”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek