Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 43 - فُصِّلَت - Page - Juz 24
﴿مَّا يُقَالُ لَكَ إِلَّا مَا قَدۡ قِيلَ لِلرُّسُلِ مِن قَبۡلِكَۚ إِنَّ رَبَّكَ لَذُو مَغۡفِرَةٖ وَذُو عِقَابٍ أَلِيمٖ ﴾
[فُصِّلَت: 43]
﴿ما يقال لك إلا ما قد قيل للرسل من قبلك إن ربك﴾ [فُصِّلَت: 43]
Khaled Ibrahim Betala “Palibe chimene chinenedwa kwa iwe (Mtumiki {s.a.w) kuchokera kwa adani ako) koma chomwe chidanenedwa kwa aneneri akale (kuchokera kwa adani awo). Ndipo Mbuye wako ndi Mwini chikhululuko chambiri (kwa amene walapa kwa Iye), ndiponso Mwini chilango chowawa (kwa yemwe wapitiriza kunyozera) |