Quran with Chichewa translation - Surah Fussilat ayat 45 - فُصِّلَت - Page - Juz 24
﴿وَلَقَدۡ ءَاتَيۡنَا مُوسَى ٱلۡكِتَٰبَ فَٱخۡتُلِفَ فِيهِۚ وَلَوۡلَا كَلِمَةٞ سَبَقَتۡ مِن رَّبِّكَ لَقُضِيَ بَيۡنَهُمۡۚ وَإِنَّهُمۡ لَفِي شَكّٖ مِّنۡهُ مُرِيبٖ ﴾
[فُصِّلَت: 45]
﴿ولقد آتينا موسى الكتاب فاختلف فيه ولولا كلمة سبقت من ربك لقضي﴾ [فُصِّلَت: 45]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ndithu tidampatsa Mûsa buku ((la Tarat)) ndipo (anthu ake) adatsutsana za ilo. Kukadapanda kutsogola liwu lochokera kwa Mbuye wako (loti adzachedwetsa chilango kwa okutsutsa) kukadaweruzidwa pakati pawo (powaononga). Ndithu iwo ali m’chikaiko choikaikira iyo (Qur’an) |