Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zukhruf ayat 26 - الزُّخرُف - Page - Juz 25
﴿وَإِذۡ قَالَ إِبۡرَٰهِيمُ لِأَبِيهِ وَقَوۡمِهِۦٓ إِنَّنِي بَرَآءٞ مِّمَّا تَعۡبُدُونَ ﴾
[الزُّخرُف: 26]
﴿وإذ قال إبراهيم لأبيه وقومه إنني براء مما تعبدون﴾ [الزُّخرُف: 26]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo (kumbuka) pamene Ibrahim adauza bambo wake ndi anthu ake (kuti): “Ndithu ine ndadzipatula ku zimene mukuzipembedzazi.” |