Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zukhruf ayat 4 - الزُّخرُف - Page - Juz 25
﴿وَإِنَّهُۥ فِيٓ أُمِّ ٱلۡكِتَٰبِ لَدَيۡنَا لَعَلِيٌّ حَكِيمٌ ﴾
[الزُّخرُف: 4]
﴿وإنه في أم الكتاب لدينا لعلي حكيم﴾ [الزُّخرُف: 4]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ndithu bukuli (Qur’an) lili m’manthu wa mabuku onse (Lawhi Mahfudh) limene lili kwa Ife; (ndipo ndi buku) lotukuka, la mawu anzeru |