Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zukhruf ayat 56 - الزُّخرُف - Page - Juz 25
﴿فَجَعَلۡنَٰهُمۡ سَلَفٗا وَمَثَلٗا لِّلۡأٓخِرِينَ ﴾
[الزُّخرُف: 56]
﴿فجعلناهم سلفا ومثلا للآخرين﴾ [الزُّخرُف: 56]
Khaled Ibrahim Betala “Tidawachita (Farawo ndi anthu ake) kukhala chitsanzo cha okanira a pambuyo pawo ndikukhala mbiri kwa anthu amene akudza |