Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zukhruf ayat 79 - الزُّخرُف - Page - Juz 25
﴿أَمۡ أَبۡرَمُوٓاْ أَمۡرٗا فَإِنَّا مُبۡرِمُونَ ﴾
[الزُّخرُف: 79]
﴿أم أبرموا أمرا فإنا مبرمون﴾ [الزُّخرُف: 79]
Khaled Ibrahim Betala “Kodi akonza bwino chikonzero (chawocho chomwe ndi chiwembu chofuna kumupha Mtumiki {s.a.w})? Ndithu nafenso ndife okonza chikonzero chabwino (cholepheretsa chiwembu chawocho) |