×

Kapena iwo amaganiza kuti Ife sitikumva zimene amabisa ndi nkhani zawo za 43:80 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Az-Zukhruf ⮕ (43:80) ayat 80 in Chichewa

43:80 Surah Az-Zukhruf ayat 80 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zukhruf ayat 80 - الزُّخرُف - Page - Juz 25

﴿أَمۡ يَحۡسَبُونَ أَنَّا لَا نَسۡمَعُ سِرَّهُمۡ وَنَجۡوَىٰهُمۚ بَلَىٰ وَرُسُلُنَا لَدَيۡهِمۡ يَكۡتُبُونَ ﴾
[الزُّخرُف: 80]

Kapena iwo amaganiza kuti Ife sitikumva zimene amabisa ndi nkhani zawo za chinsinsi? Ndithudi Ife timamva ndipo Atumwi athu amene ali pakati pawo amalemba chilichonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أم يحسبون أنا لا نسمع سرهم ونجواهم بلى ورسلنا لديهم يكتبون, باللغة نيانجا

﴿أم يحسبون أنا لا نسمع سرهم ونجواهم بلى ورسلنا لديهم يكتبون﴾ [الزُّخرُف: 80]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi akuganiza kuti sitikumva zobisa zawo ndi zonong’oneza zawo? Iyayi, (tikuzimva zonse), ndipo atumiki Athu (angelo) ali nawo pamodzi; akulemba
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek