×

Ichi ndi chivumbulutso chochokera kwa Mulungu chimene tili kulakatula kwa iwe mwachoonadi. 45:6 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Jathiyah ⮕ (45:6) ayat 6 in Chichewa

45:6 Surah Al-Jathiyah ayat 6 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jathiyah ayat 6 - الجاثِية - Page - Juz 25

﴿تِلۡكَ ءَايَٰتُ ٱللَّهِ نَتۡلُوهَا عَلَيۡكَ بِٱلۡحَقِّۖ فَبِأَيِّ حَدِيثِۭ بَعۡدَ ٱللَّهِ وَءَايَٰتِهِۦ يُؤۡمِنُونَ ﴾
[الجاثِية: 6]

Ichi ndi chivumbulutso chochokera kwa Mulungu chimene tili kulakatula kwa iwe mwachoonadi. Nanga ndi uthenga uti wa Mulungu ndi chivumbulutso chake chiti chomwe iwo akhoza kukhulupirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: تلك آيات الله نتلوها عليك بالحق فبأي حديث بعد الله وآياته يؤمنون, باللغة نيانجا

﴿تلك آيات الله نتلوها عليك بالحق فبأي حديث بعد الله وآياته يؤمنون﴾ [الجاثِية: 6]

Khaled Ibrahim Betala
“Izi ndi Ayah (ndime) za Allah; tikukuwerengera iwe mwachoonadi. Kodi ndi nkhani yanji adzaikhulupirire atapanda kulabadira nkhani ya Allah ndi Ayah Zake
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek