×

Ndi m’kasinthidwe ka usiku ndi usana ndi m’chakudya chimene amatumiza kuchokera ku 45:5 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Jathiyah ⮕ (45:5) ayat 5 in Chichewa

45:5 Surah Al-Jathiyah ayat 5 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jathiyah ayat 5 - الجاثِية - Page - Juz 25

﴿وَٱخۡتِلَٰفِ ٱلَّيۡلِ وَٱلنَّهَارِ وَمَآ أَنزَلَ ٱللَّهُ مِنَ ٱلسَّمَآءِ مِن رِّزۡقٖ فَأَحۡيَا بِهِ ٱلۡأَرۡضَ بَعۡدَ مَوۡتِهَا وَتَصۡرِيفِ ٱلرِّيَٰحِ ءَايَٰتٞ لِّقَوۡمٖ يَعۡقِلُونَ ﴾
[الجاثِية: 5]

Ndi m’kasinthidwe ka usiku ndi usana ndi m’chakudya chimene amatumiza kuchokera ku mitambo ndipo amapereka moyo ku nthaka imene idali yakufa ndipo m’kasinthidwe ka mphepo, muli zizindikiro kwa anthu ozindikira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: واختلاف الليل والنهار وما أنـزل الله من السماء من رزق فأحيا به, باللغة نيانجا

﴿واختلاف الليل والنهار وما أنـزل الله من السماء من رزق فأحيا به﴾ [الجاثِية: 5]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndi kusinthana kwa usana ndi usiku, ndi mvula imene Allah akutsitsa kuchokera kumwamba, akuukitsa nthaka ndi mvulayo, itafa (itauma), ndi kuyendetsa mphepo mosinthasintha; (zonsezi) ndi zisonyezo kwa anthu anzeru
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek