Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahqaf ayat 13 - الأحقَاف - Page - Juz 26
﴿إِنَّ ٱلَّذِينَ قَالُواْ رَبُّنَا ٱللَّهُ ثُمَّ ٱسۡتَقَٰمُواْ فَلَا خَوۡفٌ عَلَيۡهِمۡ وَلَا هُمۡ يَحۡزَنُونَ ﴾
[الأحقَاف: 13]
﴿إن الذين قالوا ربنا الله ثم استقاموا فلا خوف عليهم ولا هم﴾ [الأحقَاف: 13]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithu amene anena (kuti): “Mbuye wathu ndi Allah.” Kenako ndikulungama, sadzakhala ndi mantha (tsiku lakufa kwawo ngakhale pambuyo pake), ndiponso sadzadandaula |