Quran with Chichewa translation - Surah Muhammad ayat 1 - مُحمد - Page - Juz 26
﴿ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ وَصَدُّواْ عَن سَبِيلِ ٱللَّهِ أَضَلَّ أَعۡمَٰلَهُمۡ ﴾ 
[مُحمد: 1]
﴿الذين كفروا وصدوا عن سبيل الله أضل أعمالهم﴾ [مُحمد: 1]
| Khaled Ibrahim Betala “Amene adam’kana (Allah ndi Mthenga Wake) ndi kutsekereza anthu kuyenda panjira ya Allah (powaletsa kulowa m’Chisilamu), Allah waononga zonse zabwino zimene adachita |