Quran with Chichewa translation - Surah Muhammad ayat 14 - مُحمد - Page - Juz 26
﴿أَفَمَن كَانَ عَلَىٰ بَيِّنَةٖ مِّن رَّبِّهِۦ كَمَن زُيِّنَ لَهُۥ سُوٓءُ عَمَلِهِۦ وَٱتَّبَعُوٓاْ أَهۡوَآءَهُم ﴾
[مُحمد: 14]
﴿أفمن كان على بينة من ربه كمن زين له سوء عمله واتبعوا﴾ [مُحمد: 14]
Khaled Ibrahim Betala “Kodi angafanane, (polandira mphoto,) amene ali ndi umboni wodziwika wochokera kwa Mbuye wake, (kotero kuti nkumamumvera, ndi amene wakometsedwa ndi zochita zake zoipa natsatira zilakolako zawo) |