Quran with Chichewa translation - Surah Muhammad ayat 16 - مُحمد - Page - Juz 26
﴿وَمِنۡهُم مَّن يَسۡتَمِعُ إِلَيۡكَ حَتَّىٰٓ إِذَا خَرَجُواْ مِنۡ عِندِكَ قَالُواْ لِلَّذِينَ أُوتُواْ ٱلۡعِلۡمَ مَاذَا قَالَ ءَانِفًاۚ أُوْلَٰٓئِكَ ٱلَّذِينَ طَبَعَ ٱللَّهُ عَلَىٰ قُلُوبِهِمۡ وَٱتَّبَعُوٓاْ أَهۡوَآءَهُمۡ ﴾
[مُحمد: 16]
﴿ومنهم من يستمع إليك حتى إذا خرجوا من عندك قالوا للذين أوتوا﴾ [مُحمد: 16]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ena mwa iwo (okana Allah) amamvetsera kwa iwe, (popanda kupindula chilichonse), ndipo akachoka pamalo pakopo, amanena kwa amene apatsidwa nzeru (mwa omtsatira ake): “Kodi (Mtumiki) wanena chiyani posachedwapa?” Iwowo ndiamene Allah wawadinda m’mitima mwawo (ndi chidindo chokana Allah), ndipo amatsatira zilakolako zawo (zachabe) |