×

Ndithudi iwo amene amabwerera m’mbuyo ndi kukhalanso osakhulupirira pamene atalandira kale ulangizi, 47:25 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Muhammad ⮕ (47:25) ayat 25 in Chichewa

47:25 Surah Muhammad ayat 25 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Muhammad ayat 25 - مُحمد - Page - Juz 26

﴿إِنَّ ٱلَّذِينَ ٱرۡتَدُّواْ عَلَىٰٓ أَدۡبَٰرِهِم مِّنۢ بَعۡدِ مَا تَبَيَّنَ لَهُمُ ٱلۡهُدَى ٱلشَّيۡطَٰنُ سَوَّلَ لَهُمۡ وَأَمۡلَىٰ لَهُمۡ ﴾
[مُحمد: 25]

Ndithudi iwo amene amabwerera m’mbuyo ndi kukhalanso osakhulupirira pamene atalandira kale ulangizi, amatsogozedwa ndi Satana amene amawanamiza ndi zinthu zopanda pake

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن الذين ارتدوا على أدبارهم من بعد ما تبين لهم الهدى الشيطان, باللغة نيانجا

﴿إن الذين ارتدوا على أدبارهم من بعد ما تبين لهم الهدى الشيطان﴾ [مُحمد: 25]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu amene akubwerera m’mbuyo (kusiya chipembedzo chawo nkubwerera ku zosakhulupirira Allah) chiongoko chitawaonekera poyera satana ndiamene wawanyenga, ndipo Allah akuwapatsa nthawi
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek