Quran with Chichewa translation - Surah Muhammad ayat 9 - مُحمد - Page - Juz 26
﴿ذَٰلِكَ بِأَنَّهُمۡ كَرِهُواْ مَآ أَنزَلَ ٱللَّهُ فَأَحۡبَطَ أَعۡمَٰلَهُمۡ ﴾ 
[مُحمد: 9]
﴿ذلك بأنهم كرهوا ما أنـزل الله فأحبط أعمالهم﴾ [مُحمد: 9]
| Khaled Ibrahim Betala “Zimenezo nchifukwa chakuti iwo azida zomwe Allah adavumbulutsa (monga Qur’an ndi malamulo ake;) choncho waziononga zochita zawo |