Quran with Chichewa translation - Surah Al-Fath ayat 14 - الفَتح - Page - Juz 26
﴿وَلِلَّهِ مُلۡكُ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِۚ يَغۡفِرُ لِمَن يَشَآءُ وَيُعَذِّبُ مَن يَشَآءُۚ وَكَانَ ٱللَّهُ غَفُورٗا رَّحِيمٗا ﴾
[الفَتح: 14]
﴿ولله ملك السموات والأرض يغفر لمن يشاء ويعذب من يشاء وكان الله﴾ [الفَتح: 14]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ufumu wakumwamba ndi pansi ngwa Allah. Amakhululukira amene wamfuna (ngati atatembenukira kwa Iye) ndi kumlanga amene wamfuna (ngati sanatembenukire kwa Iye). Ndipo Allah Ngokhululuka kwambiri, Ngwachisoni chosatha |