Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma’idah ayat 103 - المَائدة - Page - Juz 7
﴿مَا جَعَلَ ٱللَّهُ مِنۢ بَحِيرَةٖ وَلَا سَآئِبَةٖ وَلَا وَصِيلَةٖ وَلَا حَامٖ وَلَٰكِنَّ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ يَفۡتَرُونَ عَلَى ٱللَّهِ ٱلۡكَذِبَۖ وَأَكۡثَرُهُمۡ لَا يَعۡقِلُونَ ﴾
[المَائدة: 103]
﴿ما جعل الله من بحيرة ولا سائبة ولا وصيلة ولا حام ولكن﴾ [المَائدة: 103]
Khaled Ibrahim Betala “Allah sadaike (kuletsedwa kwamtundu uliwonse) pa nyama yotchedwa Bahira*, ngakhale Saiba**, ngakhale Wasila***, ngakhalenso Hami****. Koma amene sadakhulupirire akumpekera Allah bodza. Ndipo ambiri a iwo sagwiritsa ntchito nzeru zawo |