×

Limene Mulungu amatsogolera, kunjira ya mtendere, onse amene amafuna chikondwerero cha Iye. 5:16 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ma’idah ⮕ (5:16) ayat 16 in Chichewa

5:16 Surah Al-Ma’idah ayat 16 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma’idah ayat 16 - المَائدة - Page - Juz 6

﴿يَهۡدِي بِهِ ٱللَّهُ مَنِ ٱتَّبَعَ رِضۡوَٰنَهُۥ سُبُلَ ٱلسَّلَٰمِ وَيُخۡرِجُهُم مِّنَ ٱلظُّلُمَٰتِ إِلَى ٱلنُّورِ بِإِذۡنِهِۦ وَيَهۡدِيهِمۡ إِلَىٰ صِرَٰطٖ مُّسۡتَقِيمٖ ﴾
[المَائدة: 16]

Limene Mulungu amatsogolera, kunjira ya mtendere, onse amene amafuna chikondwerero cha Iye. Mulungu amawatulutsa, mwachifuniro chake, kuchoka ku mdima ndi kunka kowala, ndipo amawatsogolera kunjira yoyenera

❮ Previous Next ❯

ترجمة: يهدي به الله من اتبع رضوانه سبل السلام ويخرجهم من الظلمات إلى, باللغة نيانجا

﴿يهدي به الله من اتبع رضوانه سبل السلام ويخرجهم من الظلمات إلى﴾ [المَائدة: 16]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndi bukulo Allah akuwatsogolera kunjira zamtendere amene akutsata chiyanjano chake ndikuwatulutsa mu m’dima ndi kuwaika m’kuunika mwa lamulo Lake, ndi kuwatsogolera kunjira yoongoka
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek